eBible.orgTranslationsCountries/Territories
eBible.orgTranslationsTerritories

 

Biblica® Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

Chichewa Bible

Language: [nya]ChichewaChichewa
Title:Biblica® Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa ChaleroChichewa Bible
Abbreviation:TCClID: NYABIB or nya
Copyright © 2016, 2002 Biblica, Inc.
FormatLink
Browser BibleStudy online with Browser Bible
Mobile HTMLRead Mobile HTML online
Zipped mobile HTMLnya_html.zip
ePub 3nya.epub
Amazon Kindle EPUBnya.epub
PDFPDF file list
Crosswire Sword modulenya2026eb.zip
Plain text canon only chapter filesnya_readaloud.zip
BibleWorks import (VPL) + SQLnya_vpl.zip
Browser Bible modulenya_browserBible.zip
USFXnya_usfx.zip
USFMnya_usfm.zip
XeTeXnya_xetex.zip

The Holy Bible in the Chichewa language of Malawi: Biblica® Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero


Pachiyambi Mulungu analenga kumwamba ndi dziko lapansi.

—Genesis 1:1



Salimo la Davide. Yehova ndiye mʼbusa wanga, sindidzasowa kanthu.

—Psalm 23:1



Koma muyambe mwafuna ufumu wake ndi chilungamo chake ndipo zinthu zonsezi zidzapatsidwa kwa inu.

—Matthew 6:33



“Pakuti Mulungu anakonda dziko lapansi, kotero anapereka Mwana wake wobadwa yekha, kuti aliyense wokhulupirira Iye asatayike koma akhale ndi moyo wosatha.

—John 3:16



Ndipo ife tikudziwa kuti zinthu zonse zimathandizana kuwachitira ubwino amene amakonda Mulungu, amene anayitanidwa monga mwa cholinga chake.

—Romans 8:28


Biblica® Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

The Holy Bible in the Chichewa language of Malawi: Biblica® Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

copyright © 2016, 2002 Biblica, Inc.
Language: Chichewa
Contributor: Biblica, Inc.

Ntchito ino imapezeka pansi pa Creative Commons Attribution –ShareAlike 4.0 Chilolezo cha Ponseponse (CC BY-SA). Mukafuna kuona chilolezo chimenechi, pitani pa http://creativecommons.org/licenses/by-sa/4‪.0 kapena lembani kalata ku Creative Commons, PO Box 1866, Mountain View, CA 94042, USA. 

Biblica® ndicho chizindikiro choikidwa ndi Biblica ndipo kuti mugwiritse ntchito Biblica® pafunika chilolezo cholembedwa ndi Biblica, Inc. mwini wake. Pansi pa malamulo a chilolezo cha CC BY-SA, mukhoza kukopa ndi kugawira ena ntchitoyi, mosaisintha pokhapokha ngati mukusunga chizindikiro cha Biblica® mosamala ndi mosachisintha. Mukafuna kusintha ntchitoyi kapena kuitanthauzira m’njira inayake, muyenera kuchotsa chizindikiro ichi cha Biblica®. Mukasintha, onetsani bwinobwino zimene mwasinthazo ndipo dziwitsani kuti: “Ntchito yonse ya Biblica, Inc. imene mwatengapo kagawo chabe ikupezeka mwaulere pa www.biblica.com ndi pa open.bible.”

Chidziwitso cha umwini chiyenera kuoneka pa tsamba lonena za Mutu wa Nchitoyi kapena pa tsamba lapadera lonena za umwini wa ntchitoyi motere:

Biblica® Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero™ 

Mwini © 2002, 2016 ndi Biblica, Inc. 

Biblica® Open Godʼs Word in Contemporary Chichewa™ 

Copyright © 2002, 2016 by Biblica, Inc. 

“Biblica” ndilo dzina lodziwika la ntchitoyi ku United States limene linalembetsedwa ndi Biblica mwini. Limagwiritsidwa ntchito ndi chilolezo. 

“Biblica” is a trademark registered in the United States Patent and Trademark Office by Biblica, Inc. Used with permission.\m Ntchito mwaichitayo ichitike potsatira malamulo a chilolezo chija (CC BY-SA).

Mukafuna kudziwitsa Biblica, Inc. zokhudza matanthauzidwe anu a ntchitoyi, chonde tipezeni pa https://open.bible/contact-us.

This work is made available under the Creative Commons Attribution-ShareAlike 4‪.0 International License (CC BY-SA). To view a copy of this license, visit http://creativecommons.org/licenses/by-sa/4‪.0 or send a letter to Creative Commons, PO Box 1866, Mountain View, CA 94042, USA.

Biblica® is a trademark registered by Biblica, Inc., and use of the Biblica® trademark requires the written permission of Biblica, Inc. Under the terms of the CC BY-SA license, you may copy and redistribute this unmodified work as long as you keep the Biblica® trademark intact. If you modify a copy or translate this work, thereby creating a derivative work, you must remove the Biblica® trademark. On the derivative work, you must indicate what changes you have made and attribute the work as follows: “The original work by Biblica, Inc. is available for free at www.biblica.com and open.bible.”

Notice of copyright must appear on the title or copyright page of the work as follows:

Biblica® Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero™ 

Mwini © 2002, 2016 ndi Biblica, Inc. 

Biblica® Open Godʼs Word in Contemporary Chichewa™ 

Copyright © 2002, 2016 by Biblica, Inc. 

“Biblica” ndilo dzina lodziwika la ntchitoyi ku United States limene linalembetsedwa ndi Biblica mwini. Limagwiritsidwa ntchito ndi chilolezo. 

“Biblica” is a trademark registered in the United States Patent and Trademark Office by Biblica, Inc. Used with permission.\m You must also make your derivative work available under the same license (CC BY-SA).

‪If you would like to notify Biblica, Inc. regarding your translation of this work, please contact us at https://open.bible/contact-us. 

This translation is made available to you under the terms of the Creative Commons Attribution Share-Alike license 4.0.

You have permission to share and redistribute this Bible translation in any format and to make reasonable revisions and adaptations of this translation, provided that:

Pictures included with Scriptures and other documents on this site are licensed just for use with those Scriptures and documents. For other uses, please contact the respective copyright owners.

Note that in addition to the rules above, revising and adapting God's Word involves a great responsibility to be true to God's Word. See Revelation 22:18-19.


2025-05-20

Last updated 2025-05-20